HomeTop NewsMusamangoti ali ku South Africa, izi ndi zina zomwe a Malawi akuchita...

Musamangoti ali ku South Africa, izi ndi zina zomwe a Malawi akuchita pa Sasafirika

1. Kukwatira nkhalamba za ku Joni cholinga apatsidwe citizenship. Zamanyazi

2. Kugwira ntchito kwa anthu ena ongobwera monga ma burundi, ma somali ndi ena. Hahahaha

3. Kumathera ndalama zimene apeza zikheba za pa Joni akuti chifukwa zimakhala zamiyendo yaboo. Midyomba hehehe

4. Kumangwadwa kwa mabwana akuti ulemu

5. Kugwira ntchito yomalandira 30 Rand pa tsiku. Hahahaha ndi pa Malawi zasiyana pati?

6. Kubeledwa osati liti chifukwa chogona

7. Akagula phone ya whatsapp kumangolengeza pa facebook ka phone number kawo

Subscribe to our Youtube Channel:

Must Read
Related News